1 Samueli 24:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Bwino lace Davide yemwe ananyamuka, naturuka m'phangamo, napfuulira Sauli, nati, Mbuye wanga, mfumu. Ndipo pakuceuka Sauli, Davide anaweramira nkhope yace pansi, namgwadira.

1 Samueli 24

1 Samueli 24:1-16