1 Samueli 23:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Davide ndi anthu ace anamuka ku Keila, naponyana ndi Afilisti, natenga ng'ombe zao, nawapha ndi kuwapulula kwambiri Motero Davide analanditsa okhala m'Keila.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:1-7