1 Samueli 23:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Sauli anabwerera polondola Davide, nakakomana ndi Afilisti; cifukwa cace anachula dzina lace la malo aja, Thanthwe lolekanitsa.

1 Samueli 23

1 Samueli 23:20-29