1 Samueli 22:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakumva Sauli kuti anadziwika Davide, ndi anthu ace akukhala naye, Sauti analikukhala m'Gibeya, patsinde pa mtengo wa kumsanje, m'dzanja lace munali mkondo wace, ndi anyamata ace onse anaimirira pali iye.

1 Samueli 22

1 Samueli 22:1-9