1 Samueli 22:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakantha Nobi ndiwo mudzi wa ansembe ndi lupanga lakuthwa, anthu amuna ndi akazi, ana ndi makanda, ng'ombe ndi aburu, ndi nkhosa, ndi lupanga lakuthwa.

1 Samueli 22

1 Samueli 22:15-20