1 Samueli 22:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahimeleki anayankha mfumu, nati, Ndipo ndani mwa anyamata anu onse ali wokhulupirika ngati Davide amene, mkamwini wa mfumu; wakuyenda mu uphungu wanu, nalemekezeka m'nyumba mwanu?

1 Samueli 22

1 Samueli 22:5-19