1 Samueli 22:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu anatuma mthenga kukaitana Ahimeleki wansembeyo, mwana wa Ahitubu, ndi banja lonse la atate wace, ansembe a ku Nobi; ndipo iwo onse anafika kwa mfumu.

1 Samueli 22

1 Samueli 22:8-15