1 Samueli 21:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati wansembeyo, Lupanga la Goliate Mfilisti munamuphayo m'cigwa ca Ela, onani-liripo lokulunga m'nsaru, kumbuyo kwa efodi; mukafuna kutenga limenelo, tengani; popeza pano palibe lina, Ndipo Davide anati, Palibe lina lotere longa lijalo, ndipatseni.

1 Samueli 21

1 Samueli 21:7-15