1 Samueli 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco wansembeyo anampatsa mkate wopatulika, popeza panalibe mkate wina, koma mkate woonekera, umene adaucotsa pamaso pa Yehova, kuti akaike mkate wotentha tsiku lomwelo anacotsa winawo.

1 Samueli 21

1 Samueli 21:5-9