1 Samueli 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atate wako akandifuna pang'ono ponse, unene kuti, Davide anandiumirira ndimlole athamangire kwao ku Betelehemu, pakuti kumeneko kuli nsembe ya pacaka ya banja lao lonse.

1 Samueli 20

1 Samueli 20:1-9