1 Samueli 20:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani ananena kwa Davide, Muka mumtendere, popeza tonsefe tinalumbira m'dzina la Yehova, kuti, Yehova adzakhala pakati pa ine ndi iwe, ndi pakati pa mbeu yanga ndi mbeu yako, nthawi zamuyaya.

1 Samueli 20

1 Samueli 20:37-43