1 Samueli 20:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamatayo atafika pa malo a mubvi umene Jonatani anauponya, Jonatani anapfuulira mnyamatayo, nati, Mubviwo suli m'tsogolo mwako kodi?

1 Samueli 20

1 Samueli 20:27-42