1 Samueli 20:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Jonatani anauka pagome wolunda ndithu, osadya kanthu tsiku laciwiri la mwezi, pakuti mtima wace unali ndi cisoni cifukwa ca Davide, popeza atate wace anamcititsa manyazi.

1 Samueli 20

1 Samueli 20:33-36