1 Samueli 2:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzali kuti yense wakusiyidwa wa m'banja lako adzabwera kwa iye nadzawerama ndi kupempha ndalama ndi cakudya, nadzati, Mundipatsetu nchito yina ya wansembe, kuti ndikaona kakudya.

1 Samueli 2

1 Samueli 2:32-36