1 Samueli 2:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anafika kwa Eli munthu wa Mulungu, nanena naye, Atero Yehova, Kodi Ine ndinadziulula kwa banja la kholo lako, muja anali m'Aigupto, m'nyumba ya Farao?

1 Samueli 2

1 Samueli 2:18-28