1 Samueli 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eli anadalitsa Elikana ndi mkazi wace, nati, Yehova akupatse mbeu ndi mkazi uyu m'malo mwa iye amene munampempha kwa Yehova. Ndipo iwowa anabwera kwao.

1 Samueli 2

1 Samueli 2:11-24