1 Samueli 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati munthu akanena naye, Koma adzatentha mafuta tsopano apa, atatha, utenge monga mtima wako ufuna; uyo akanena naye, lai, koma undipatsire iyo tsopanoli, ukapanda kutero ndidzailanda.

1 Samueli 2

1 Samueli 2:12-19