1 Samueli 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hana anapemphera, natiMtima wanga umyuka mokondwera kwa Yehova,Nyanga yanga yakwezeka mwa Yehova;Pakamwa panga pakula kwa adani anga;Popeza ndikondwera m'cipulumutsocanu.

1 Samueli 2

1 Samueli 2:1-7