1 Samueli 19:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Jonatani anaitana Davide, namuuza zonsezi. Ndipo Jonatani anafika naye Davide kwa Sauli, iye nakhalanso pamaso pace monga kale.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:4-15