1 Samueli 19:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo iyenso anamuka ku Rama, nafika ku citsime cacikuru ciri ku Seku, nafunsa Dati, Samueli ndi Davide ali kuti? Ndipo wina anati, Taonani, ali ku Nayoti m'Rama.

1 Samueli 19

1 Samueli 19:12-24