1 Samueli 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Jonatani mwana wa Sauli anakondwera kwambiri ndi Davide. Ndipo Jonatani anauza Davide, nati, Sauli atate wanga alikufuna kukupha; cifukwa cace tsono ucenjere m'mawa, mukhale m'malo mosadziwika, nubisale;

1 Samueli 19

1 Samueli 19:1-8