1 Samueli 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakutsiriza iye kulankhula ndi Sauli, mtima wa Jonatani unalumikizika ndi mtima wa Davide, ndipo Jonatani anamkonda iye monga moyo wa iye yekha.

1 Samueli 18

1 Samueli 18:1-3