1 Samueli 17:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anatenga mutu wa Mfilistiyo, napita nao ku Yerusalemu; koma zida zace anazisunga m'hema wace.

1 Samueli 17

1 Samueli 17:44-55