1 Samueli 17:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero Davide anathamanga naima pa Mfilistiyo, nagwira lupanga lace, nalisolola m'cimace, namtsiriza nadula nalo mutu wace. Ndipo pakuona Afilisti kuti ciwinda cao cidafa, anathawa.

1 Samueli 17

1 Samueli 17:46-56