1 Samueli 17:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Davide, Yehova wakundipulumutsa pa mphamvu ya mkango, ndi mphamvu ya cimbalangondo, Iyeyu adzandipulumutsa m'dzanja la Mfilisti uyu, Ndipo Sauli anati kwa Davide, Muka, Yehova akhale nawe.

1 Samueli 17

1 Samueli 17:29-45