1 Samueli 17:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mene iye anali cilankhulire nao, onani cinakwerako ciwindaco, Mfilisti wa ku Gati, dzina lace ndiye Goliate, woturuka pakati pa mipambo ya Afilisti, nalankhula monga mau omwe aja; ndipo Davide anawamva.

1 Samueli 17

1 Samueli 17:20-27