1 Samueli 16:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anacita cimene Yehova ananena, nadza ku Betelehemu. Ndipo akuru a mudziwo anadza kukomana naye monthunthumira, nati, Mubwera ndi mtendere kodi?

1 Samueli 16

1 Samueli 16:3-7