1 Samueli 16:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jese anapititsapo ana ace amuna asanu ndi awiri. Koma Samueli anati kwa Jese, Yehova sanawasankha awa.

1 Samueli 16

1 Samueli 16:8-13