1 Samueli 15:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli anati, Bwerani naye kwa ine kuno Agagi mfumu ya Aamaleki. Ndipo Agagi anabwera kwa iye mokondwera. Nati Agagi, Zoonadi kuwawa kwa imfa kunapitirira.

1 Samueli 15

1 Samueli 15:25-35