1 Samueli 15:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo iye anati, Ndinacimwa, koma mundicitire ulemu tsopano pamaso pa akuru a anthu anga, ndi pamaso pa Israyeli, nimubwerere pamodzi ndi ine, kuti ndikalambire Yehova Mulungu wanu.

1 Samueli 15

1 Samueli 15:21-35