1 Samueli 15:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anati kwa Samueli, Ndinacimwa; pakuti ndinalumpha lamulo la Yehova, ndi mau anu omwe; cifukwa ndinaopa anthuwo, ndi kumvera mau ao.

1 Samueli 15

1 Samueli 15:17-26