1 Samueli 15:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anthuwo anatengako zowawanya, nkhosa ndi ng'ombe, zoposa za zija tidayenera kuziononga, kuziphera nsembe kwa Yehova Mulungu wanu ku Giligala.

1 Samueli 15

1 Samueli 15:17-25