1 Samueli 14:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a Sauli ndiwo Jonatani, ndi Isivi, ndi Malikisuwa; ndi maina a ana akazi ace awm ndi awa: dzina la woyamba ndiye Merabu, ndi dzina la mng'ono wace ndiye Mikala;

1 Samueli 14

1 Samueli 14:47-52