1 Samueli 14:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananena ndi Aisrayeli onse, Inu mukhale mbali yina, ndipo me ndi Jonatani mwana wanga tidzakhala mbali yinanso. Ndipo anthuwo ananena ndi Sauli, Citani cimene cikukomerani.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:31-43