1 Samueli 14:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wina wa anthuwo anayankha, nati, Atate wanu analangiza anthu kolimba ndi lumbiro, ndi kuti, Wotembereredwa iye wakudya lero cakudya. Ndipo anthuwo analema.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:27-32