1 Samueli 14:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aisrayeli anasauka tsiku lija; pakuti Sauli anawalumbirira, kuti, Atembereredwe iye wakudya kanthu kufikira madzulo, ndikabwezere cilango adani anga. Motero anthu onse anakhala opanda kudya.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:23-26