1 Samueli 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Sauli ananena ndi anthu amene anali naye, Awerenge tsopano, kuti tizindikire anaticokera ndani. Ndipo pamene anawerenga, onani Jonatani ndi wonyamula zida zace panalibe.

1 Samueli 14

1 Samueli 14:11-20