1 Samueli 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ahebri ena anaoloka Yordano nafika ku dziko la Gadi ndi Gileadi; koma Sauli akali ku Giligala, ndipo anthu onse anamtsata ndi kunthunthumira.

1 Samueli 13

1 Samueli 13:4-15