1 Samueli 13:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aisrayeli onse anamva kunena kuti Sauli anathyola kaboma ka Afilisti, ndi kuti Afilisti anyansidwa ndi Aisrayeli. Ndipo anthuwo anasonkhana kwa Sauli ku Giligala.

1 Samueli 13

1 Samueli 13:1-12