1 Samueli 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma tsopano ufumu wanu sudzakhala cikhalire; Yehova wadzifunira munthu wa pamtima pace; ndipo Yehova wamuika iye akhale mtsogoleri wa anthu ace, cifukwa inu simunasunga cimene Yehova anakulamulirani.

1 Samueli 13

1 Samueli 13:8-23