1 Samueli 12:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananena nao, Yehova ali mboni yanu, ndi wodzozedwa wace ali mboni lero kuti simunapeza kanthu m'dzanja langa, Nati iwo, iye ali mboni.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:3-6