1 Samueli 12:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mumuope Yehova, ndi kumtumikira koona, ndi mtima wanu wonse; lingalirani zinthu zazikuruzo iye anakucitirani.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:22-25