1 Samueli 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova sadzasiya anthu ace cifukwa ca dzina lace lalikuru; pakuti kudamkomera Yehova kukuyesani inu anthu a iye yekha.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:12-25