1 Samueli 12:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli ananena kwa anthuwo, Musaope; munacitadi coipa ici conse, koma musaleka kutsata Yehova, koma mutumikire Yehova ndi mtima wanu wonse;

1 Samueli 12

1 Samueli 12:16-25