1 Samueli 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mukapanda kumvera mau a Yehova, ndi kupikisana ndi lamulo la Yehova, dzanja la Yehova lidzatsutsana nanu, monga linatsutsana ndi makolo anu.

1 Samueli 12

1 Samueli 12:5-23