1 Samueli 11:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mzimu wa Mulungu unamgwera Sauli mwamphamvu, pamene anamva mau awa, ndi mkwiyo wace unayaka kwambiri.

1 Samueli 11

1 Samueli 11:5-10