1 Samueli 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Samueli ananena ndi anthu onse, Mumuona kodi iye amene Yehova anamsankha, kuti palibe wina wakufanana naye pakati pa anthu onse? Ndipo anthu onse anapfuula, kuti, Akhale ndi moyo mfumuyo.

1 Samueli 10

1 Samueli 10:23-26