1 Samueli 1:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mwamuna wace Elikana anati kwa iye, Hana, umaliriranji? ndipo umakaniranji kudya? ndipo mtima wako uwawa ninji? Ine sindiri wakuposa ana khumi kwa iwe kodi?

1 Samueli 1

1 Samueli 1:1-14