1 Samueli 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iyeyu anali nao akazi awiri; winayo dzina lace ndi Hana, mnzace dzina lace ndi Penina. Ndipo Penina anaona ana, koma Hana anali wouma.

1 Samueli 1

1 Samueli 1:1-8