1 Samueli 1:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hana anayankha, nati, Iai, mbuyanga. Ine ndiri mkazi wa mtima wacisoni; sindinamwa vinyo kapena cakumwa cowawa, koma ndinatsanulira mtima wanga pamaso pa Yehova.

1 Samueli 1

1 Samueli 1:10-22